bible-chichewa
Version:
The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.
1 lines • 886 B
JSON
["Muimbireni Yehova nyimbo yatsopano;popeza anachita zodabwitsa:Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera,zinamchitira chipulumutso.","Yehova anawadziwitsira chipulumutso chake;anaonetsera chilungamo chake pamaso pa amitundu.","Anakumbukira chifundo chake ndi chikhulupiriko chakekunyumba ya Israele;malekezero onse a dziko lapansianaona chipulumutso cha Mulungu wathu.","Fuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi;kuwitsani ndi kufuulira mokondwera;inde, imbirani zomlemekeza.","Muimbireni Yehova zomlemekeza ndi zeze;ndi zeze ndi mau a salimo.","Fuulani pamaso pa Mfumu Yehova,ndi mbetete ndi liu la lipenga.","Nyanja ifuule ndi kudzala kwake;dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhalamo;","mitsinje iombe manja;mapiri afuule pamodzi mokondwera.","Pamaso pa Yehova, popeza akudza kudzaweruza dziko lapansi;adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi chilungamo,ndipo mitundu ya anthu molunjika."]