bible-chichewa
Version:
The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.
1 lines • 517 B
JSON
["Yehova achita ufumu; wadziveka ndi ukulu;wadziveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'chuuno;dziko lomwe lokhalamo anthu likhakizika, silidzagwedezeka.","Mpando wachifumu wanu ukhazikika kuyambira kale lija;Inu ndinu wosayambira ndi kale lomwe.","Mitsinje ikweza, Yehova,mitsinje ikweza mkokomo wao;mitsinje ikweza mafunde ao.","Yehova Wam'mwamba ndiye wamphamvu,wakuposa mkokomo wa madzi ambiri,ndi mafunde olimba a nyanja.","Mboni zanu zivomerezeka ndithu;chiyero chiyenera nyumba yanu,Yehova, kunthawi za muyaya."]