bible-chichewa
Version:
The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.
1 lines • 850 B
JSON
["Tikuyamikani Inu, Mulungu;tiyamika, pakuti dzina lanu lili pafupi;afotokozera zodabwitsa zanu.","Pakuona nyengo yake ndidzaweruza molunjika.","Lasungunuka dziko lapansi, ndi onse okhalamo;ndinachirika mizati yake.","Ndinati kwa odzitamandira,musamachita zodzitamandira;ndi kwa oipa, Musamakweza nyanga;","musamakwezetsa nyanga yanu;musamalankhula ndi khosi louma.","Pakuti kukuzaku sikuchokera kum'mawa,kapena kumadzulo, kapena kuchipululu.","Pakuti Mulungu ndiye woweruza;achepsa wina, nakuza wina.","Pakuti m'dzanja la Yehova muli chikho;ndi vinyo wake achita thovu;chidzala ndi zosanganizira, ndipo atsanulako.Indedi, oipa onse a pa dziko lapansi adzamwanadzagugudiza nsenga zake.","Koma ine ndidzalalikira kosalekeza,ndidzaimbira zomlemekeza Mulungu wa Yakobo.","Ndipo ndidzatseteka nyanga zonse za oipa;koma nyanga za wolungama zidzakwezeka."]