UNPKG

bible-chichewa

Version:

The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.

1 lines 576 B
["Yehova ndiye mbusa wanga; sindidzasowa.","Andigonetsa kubusa lamsipu,anditsogolera kumadzi odikha.","Atsitsimutsa moyo wanga;anditsogolera m'mabande a chilungamo, chifukwa cha dzina lake.","Inde, ndingakhale ndiyenda m'chigwa cha mthunzi wa imfa,sindidzaopa choipa; pakuti Inu muli ndi ine;chibonga chanu ndi ndodo yanu, izi zindisangalatsa ine.","Mundiyalikira gome pamaso panga m'kuona kwa adani anga;mwandidzoza mutu wanga mafuta; chikho changa chisefuka.","Inde ukoma ndi chifundo zidzanditsatamasiku onse a moyo wanga,ndipo ndidzakhala m'nyumba ya Yehova masiku onse."]