bible-chichewa
Version:
The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.
1 lines • 953 B
JSON
["Aphokoseranji amitundu,nalingiriranji anthu zopanda pake?","Adzikhazikitsa mafumu a dziko lapansi,nachita upo akulu pamodzi,Kutsutsana naye Yehova, ndi Wodzozedwa wake, ndi kuti,","Tidule zomangira zao,titaye nsinga zao.","Wokhala m'mwambayo adzaseka;Ambuye adzawanyoza.","Pomwepo adzalankhula nao mu mkwiyo wake,nadzawaopsa m'ukali wake.","Koma Ine ndadzoza mfumu yangaPa Ziyoni, phiri langa loyera.","Ndidzauza za chitsimikizo:Yehova ananena ndi Ine,Iwe ndiwe Mwana wanga; Ine lero ndakubala.","Undifunse, ndipo ndidzakupatsa amitunduakhale cholowa chako,ndi malekezero a dziko lapansi akhale akoako.","Udzawathyola ndi ndodo yachitsulo;udzawaphwanya monga mbiya ya woumba.","Tsono, mafumu inu, chitani mwanzeru;langikani, oweruza inu a dziko lapansi.","Tumikirani Yehova ndi mantha,ndipo kondwerani ndi chinthenthe.","Mpsompsoneni Mwanayo, kuti angakwiye,ndipo mungatayike m'njiraukayaka pang'ono pokha mkwiyo wake.Odala onse akumkhulupirira Iye."]