bible-chichewa
Version:
The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.
1 lines • 834 B
JSON
["Ku mitsinje ya ku Babiloni,kumeneko tinakhala pansi, inde tinalira,pokumbukira Ziyoni.","Pa msondodzi uli m'mwemotinapachika mazeze athu.","Popeza pamenepo akutigwirawo anatifunsa nyimbondipo akutizunza anafuna tisekere,ndi kuti, Mutiimbire nyimbo imodzi ya ku Ziyoni.","Tidati, Tidzaimba bwanji nyimbo ya Yehovam'dziko lachilendo?","Ndikakuiwalani, Yerusalemu,dzanja lamanja langa liiwale luso lake.","Lilime langa limamatike kunsaya zanga,ndikapanda kukumbukira inu;ndikapanda kusankha Yerusalemukoposa chimwemwe changa chopambana.","Yehova, kumbukirani ana a Edomutsiku la Yerusalemu;amene adati, Gamulani, gamulani,kufikira maziko ake.","Mwana wamkazi wa ku Babiloni,iwe amene udzapasulidwa;wodala iye amene adzakubwezera chilangomonga umo unatichitira ife.","Wodala iye amene adzagwira makanda ako,ndi kuwaphwanya pathanthwe."]