UNPKG

bible-chichewa

Version:

The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.

1 lines 536 B
["M'mozamamo ndinakufuulirani, Yehova.","Ambuye, imvani liu langa;makutu anu akhale chimvereremau a kupemba kwanga.","Mukasunga mphulupulu, Yehova,adzakhala chilili ndani, Ambuye?","Koma kwa Inu kuli chikhululukiro,kuti akuopeni.","Ndilindira Yehova, moyo wanga ulindira,ndiyembekeza mau ake.","Moyo wanga uyang'anira Ambuye,koposa alonda matanda kucha;inde koposa alonda matanda kucha.","Israele, uyembekezere Yehova;chifukwa kwa Yehova kuli chifundo,kwaonso kuchulukira chiombolo.","Ndipo adzaombola Israeleku mphulupulu zake zonse."]