UNPKG

bible-chichewa

Version:

The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.

1 lines 456 B
["Ndinafuulira kwa Yehova mu msauko wanga,ndipo anandivomereza.","Yehova, landitsani moyo wanga kumilomo ya mabodza,ndi kulilime lonyenga.","Adzakuninkhanji, adzakuonjezeranji,lilime lonyenga iwe?","Mivi yakuthwa ya chiphona,ndi makala tsanya.","Tsoka ine, kuti ndili mlendo m'Meseki,kuti ndigonera m'mahema a Kedara!","Moyo wanga unakhalitsa nthawipamodzi ndi iye wakudana nao mtendere.","Ine ndikuti, Mtendere;koma polankhula ine, iwowa akuti, Nkhondo."]