bible-chichewa
Version:
The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.
1 lines • 627 B
JSON
["Aleluya;Lemekezani, inu atumiki a Yehova;lemekezani dzina la Yehova.","Lodala dzina la Yehova Kuyambira tsopano kufikira kosatha.","Chitulukire dzuwa kufikira kulowa kwakelilemekezedwe dzina la Yehova.","Yehova akwezeka pamwamba pa amitundu onse,ulemerero wake pamwambamwamba.","Akunga Yehova Mulungu wathu ndani?Amene akhala pamwamba patali,","nadzichepetsa apenyezam'mwamba ndi za pa dziko lapansi.","Amene autsa wosauka kumchotsa kufumbi,nakweza waumphawi kumchotsa kudzala.","Kuti amkhalitse pamodzi ndi akulu,pamodzi ndi akulu a anthu ake.","Asungitsa nyumba mkazi wosaona mwana,akhale mai wokondwera ndi ana. Aleluya."]