UNPKG

bible-chichewa

Version:

The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.

1 lines 682 B
["Yehova ananena kwa Ambuye wanga,Khalani pa dzanja lamanja langa,kufikira nditaika adani anu chopondapo mapazi anu.","Yehova adzatumiza ndodo ya mphamvu yanu kuchokera ku Ziyoni;chitani ufumu pakati pa adani anu.","Anthu anu adzadzipereka eni ake tsiku la chamuna chanu:M'moyera mokometsetsa, mobadwira matanda kucha,muli nao mame a ubwana wanu.","Yehova walumbira, ndipo sadzasintha,Inu ndinu wansembe kosathamonga mwa chilongosoko cha Melkizedeki.","Yehova pa dzanja lamanja lakoadzaphwanya mafumu tsiku la mkwiyo wake.","Adzaweruza mwa amitundu,adzadzaza dziko ndi mitembo;adzaphwanya mitu m'maiko ambiri.","Adzamwa kumtsinje wa panjira;chifukwa chake adzaweramutsa mutu wake."]