bible-chichewa
Version:
The Chichewa Bible npm package is an open source project that provides developers with a convenient way to access and work with the Chichewa translation of the Bible within their Node.js applications.
1 lines • 662 B
JSON
["Ndakhulupirira Yehova,mutani nkunena kwa moyo wanga,Thawirani kuphiri lanu ngati mbalame?","Pakuti, onani, oipa akoka uta,apiringidza muvi wao pansinga,kuwaponyera mumdima oongoka mtima.","Akapasuka maziko,wolungama angachitenji?","Yehova ali m'Kachisi wake woyera,Yehova, mpando wachifumu wake uli m'Mwamba;apenyerera ndi maso ake, ayesa ana a anthu ndi zikope zake.","Yehova ayesa wolungama mtima,koma moyo wake umuda woipa ndi iye wakukonda chiwawa.","Adzagwetsa pwatapwata misampha pa oipa;moto ndi miyala ya sulufure,ndi mphepo yoopsa zidzawagawikira m'chikho chao.","Pakuti Yehova ndiye wolungama; akonda zolungama;woongoka mtima adzapenya nkhope yake."]